Malamulo Ogwiritsira Ntchito

Kugwiritsa nchito ndi kuonetsanso zolemba zathu

Mauthenga a uzimu athu olembedwa amaperekedwa apa kuti muagwiritse ntchito. Khalani omasuka kusindikiza ndi kugwiritsa ntchito pamene mukugawana Uthenga Wabwino ndi apabanja, abwenzi, ndi ena omwe mumadziwana nawo. Komanso masukani kuaikanso pa webusaiti yanu. Zonse zomwe tikupempha ndikuti asasinthidwe komanso kuti mupereke cholumikizanitsa ku webusaiti yathu.

Ikani cholumikizanitsa ku webusaiti yanu

Chitani copy ndi paste HTML munsimu mu webusaiti yanu kuti ogwiritsa ntchitowo akhale ndi cholumikizanitsa ku zolemba zathu.

<a href="https://www.uthengawauzimu.org">Dinani apa kuwerenga zolemba za Buku Lopatulika.</a>