Gospel Tract and Bible Society

Takulandirani ku Gospel Tract and Bible Society. Cholinga cha Gospel Tract and Bible Society ndi kugawira dziko lapansi Uthenga Wabwino wa Chipulumutso mwa chisomo, kupyolera mwa chikhulupiriro mwa Yesu Khristu, motero kumathandiza kukwaniritsa ntchito ya Khristu.

Lumikizanani nafe.

Ngati muli ndi mafunso okhudza Buku Lopatulika kapena mukufuna kulumikizana ndi wina za mauthenga awa, lembani uthenga munsimu. Mukhozanso kupempha makope aulere a mauthenga a uzimuwa kuti mutumiziridwe kuti muwerenge ndi kugawa.


Pezani mauthenga olembedwa.